Yesaya 50:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza.+ N’chifukwa chake sindidzamva kuti ndanyozeka. Pa chifukwa chimenechi ndalimbitsa nkhope yanga ngati mwala wa nsangalabwi, ndipo ndikudziwa kuti sindidzachita manyazi.+ Zekariya 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anaumitsa mtima wawo+ ngati mwala wolimba kwambiri kuti asamvere malamulo+ ndi mawu a Yehova wa makamu, amene anawatumizira mwa mzimu wake+ kudzera mwa aneneri akale.+ Choncho Yehova wa makamu anakwiya kwambiri.”+
7 Koma Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, adzandithandiza.+ N’chifukwa chake sindidzamva kuti ndanyozeka. Pa chifukwa chimenechi ndalimbitsa nkhope yanga ngati mwala wa nsangalabwi, ndipo ndikudziwa kuti sindidzachita manyazi.+
12 Iwo anaumitsa mtima wawo+ ngati mwala wolimba kwambiri kuti asamvere malamulo+ ndi mawu a Yehova wa makamu, amene anawatumizira mwa mzimu wake+ kudzera mwa aneneri akale.+ Choncho Yehova wa makamu anakwiya kwambiri.”+