30 Koma munaleza nawo mtima kwa zaka zambiri+ ndipo munapitirizabe kuwachenjeza+ mwa mzimu wanu potumiza aneneri anu, koma iwo sanamvere.+ Pamapeto pake munawapereka m’manja mwa mitundu ya anthu ya m’dzikolo.+
51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+