Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 106:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Mobwerezabwereza anali kuwapereka m’manja mwa anthu a mitundu ina,+

      Kuti anthu odana nawo awalamulire,+

  • Yesaya 42:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Ndani wachititsa kuti Yakobo angokhala zofunkha ndiponso kupereka Isiraeli kwa anthu olanda? Kodi si Yehova amene iwo am’chimwira, amene sanafune kuyenda m’njira zake ndipo sanasunge malamulo ake?+

  • Yeremiya 40:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Yehova ananena za tsoka limeneli moti anatsimikiza kukwaniritsa zimene ananenazo. Anatero chifukwa anthu inu munachimwira Yehova ndipo simunamvere mawu ake. Choncho monga mmene ukuoneramu, zimenezi zachitikadi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena