Yeremiya 50:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu anga adyedwa ndi aliyense wowapeza,+ ndipo adani awo anena kuti,+ ‘Sitipalamula mlandu uliwonse, chifukwa iwo achimwira Yehova,+ malo okhalamo chilungamo.+ Achimwira Yehova chiyembekezo cha makolo awo.’”+ Danieli 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu onse a mu Isiraeli aphwanya malamulo anu ndipo apatuka mwa kusamvera mawu anu.+ Choncho inu mwatitsanulira temberero ndi malumbiro+ amene analembedwa m’chilamulo cha Mose, mtumiki wa Mulungu woona, pakuti takuchimwirani. Aroma 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+
7 Anthu anga adyedwa ndi aliyense wowapeza,+ ndipo adani awo anena kuti,+ ‘Sitipalamula mlandu uliwonse, chifukwa iwo achimwira Yehova,+ malo okhalamo chilungamo.+ Achimwira Yehova chiyembekezo cha makolo awo.’”+
11 Anthu onse a mu Isiraeli aphwanya malamulo anu ndipo apatuka mwa kusamvera mawu anu.+ Choncho inu mwatitsanulira temberero ndi malumbiro+ amene analembedwa m’chilamulo cha Mose, mtumiki wa Mulungu woona, pakuti takuchimwirani.
5 Koma chifukwa chakuti ndiwe wosafuna kusintha khalidwe+ ndiponso wa mtima wosalapa,+ ukudzisungira mkwiyo wa Mulungu.+ Mulungu adzasonyeza mkwiyo+ umenewu pa tsiku loulula+ chiweruzo chake cholungama.+