Mateyu 10:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndipotu tsitsi lenilenilo la m’mutu mwanu amaliwerenga.+ Luka 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Komatu ngakhale tsitsi limodzi lokha+ la m’mutu mwanu silidzawonongeka ayi. Machitidwe 27:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho ndikukulimbikitsani kuti mudye kuti zinthu zikuyendereni bwino. Pakuti ngakhale tsitsi+ limodzi la kumutu kwa aliyense wa inu siliwonongeka.”
34 Choncho ndikukulimbikitsani kuti mudye kuti zinthu zikuyendereni bwino. Pakuti ngakhale tsitsi+ limodzi la kumutu kwa aliyense wa inu siliwonongeka.”