Danieli 4:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Popeza ananena kuti asiye chitsa cha mtengowo,+ inu mudzayambiranso kulamulira mu ufumu wanu mutadziwa kuti Mulungu ndiye akulamulira kumwamba.+
26 “‘Popeza ananena kuti asiye chitsa cha mtengowo,+ inu mudzayambiranso kulamulira mu ufumu wanu mutadziwa kuti Mulungu ndiye akulamulira kumwamba.+