Mateyu 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kanjere kameneka ndi kakang’ono kwambiri mwa njere zonse, koma kakamera kamakula kwambiri kuposa mbewu zonse zakudimba ndipo umakhala mtengo, moti mbalame zam’mlengalenga+ zimabwera kudzapeza malo okhala munthambi zake.”+
32 Kanjere kameneka ndi kakang’ono kwambiri mwa njere zonse, koma kakamera kamakula kwambiri kuposa mbewu zonse zakudimba ndipo umakhala mtengo, moti mbalame zam’mlengalenga+ zimabwera kudzapeza malo okhala munthambi zake.”+