Danieli 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iwo anauza mfumu Nebukadinezara kuti: “Inu mfumu, mukhale ndi moyo mpaka kalekale.+