Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pamenepo ndinayankha mfumuyo kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Kodi nkhope yanga ilekerenji kukhala yachisoni pamene mzinda+ umene makolo anga+ anaikidwako uli bwinja ndipo zipata zake zinatenthedwa ndi moto?”+

  • Danieli 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pamenepo Akasidi anayankha mfumu m’chinenero cha Chiaramu+ kuti: “Inu mfumu mukhale ndi moyo mpaka kalekale.*+ Tiuzeni ife atumiki anu zimene mwalota ndipo tikumasulirani malotowo.”+

  • Danieli 5:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano popeza mfumukazi inamva mawu a mfumu ndi a nduna zake, inalowa m’chipinda chimene anali kuchitira phwandolo. Mfumukaziyo inati: “Inu mfumu, mukhale ndi moyo mpaka kalekale.+ Musachite mantha komanso nkhope yanu isasinthe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena