1 Mafumu 1:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Kenako Bati-seba anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi+ pamaso pa mfumu, n’kunena kuti: “Mbuyanga Mfumu Davide akhale ndi moyo mpaka kalekale!”*+ Danieli 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pamenepo Akasidi anayankha mfumu m’chinenero cha Chiaramu+ kuti: “Inu mfumu mukhale ndi moyo mpaka kalekale.*+ Tiuzeni ife atumiki anu zimene mwalota ndipo tikumasulirani malotowo.”+
31 Kenako Bati-seba anagwada n’kuwerama mpaka nkhope yake pansi+ pamaso pa mfumu, n’kunena kuti: “Mbuyanga Mfumu Davide akhale ndi moyo mpaka kalekale!”*+
4 Pamenepo Akasidi anayankha mfumu m’chinenero cha Chiaramu+ kuti: “Inu mfumu mukhale ndi moyo mpaka kalekale.*+ Tiuzeni ife atumiki anu zimene mwalota ndipo tikumasulirani malotowo.”+