Ezara 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Bisilamu, Mitiredati, Tabeeli, ndi anzake ena onse analemba kalata kwa Aritasasita mfumu ya Perisiya m’masiku a mfumuyo. Kalatayo anaimasulira m’Chiaramu n’kuilemba m’zilembo za Chiaramu.+ Yesaya 36:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Eliyakimu,+ Sebina,+ ndi Yowa+ anauza Rabisake+ kuti: “Chonde lankhulani ndi ife atumiki anu m’chilankhulo cha Asiriya+ chifukwa timachimva. Musalankhule nafe m’chilankhulo cha Ayuda,+ kuti anthu amene ali pamakomawa asamve.”+
7 Bisilamu, Mitiredati, Tabeeli, ndi anzake ena onse analemba kalata kwa Aritasasita mfumu ya Perisiya m’masiku a mfumuyo. Kalatayo anaimasulira m’Chiaramu n’kuilemba m’zilembo za Chiaramu.+
11 Pamenepo Eliyakimu,+ Sebina,+ ndi Yowa+ anauza Rabisake+ kuti: “Chonde lankhulani ndi ife atumiki anu m’chilankhulo cha Asiriya+ chifukwa timachimva. Musalankhule nafe m’chilankhulo cha Ayuda,+ kuti anthu amene ali pamakomawa asamve.”+