1 Mafumu 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Bati-seba anagwada n’kuweramira pansi+ pamaso pa mfumu. Mfumuyo inati: “Ukufuna kupempha chiyani?”+
16 Bati-seba anagwada n’kuweramira pansi+ pamaso pa mfumu. Mfumuyo inati: “Ukufuna kupempha chiyani?”+