Danieli 2:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Pa chifukwa chimenechi, mfumu inamukweza pa udindo Danieli+ ndipo inamupatsa mphatso zambiri. Inamuikanso kukhala wolamulira chigawo chonse cha Babulo+ ndiponso wamkulu wa akuluakulu a boma* oyang’anira amuna onse anzeru a m’Babulo. Danieli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “‘Iwe Belitesazara mkulu wa ansembe ochita zamatsenga,+ ndikudziwa bwino kuti mzimu wa milungu yoyera uli mwa iwe+ ndipo palibe chinsinsi chimene umavutika nacho.+ Chotero ndiuze zimene ndinaona m’maloto anga ndi kumasulira kwake.+
48 Pa chifukwa chimenechi, mfumu inamukweza pa udindo Danieli+ ndipo inamupatsa mphatso zambiri. Inamuikanso kukhala wolamulira chigawo chonse cha Babulo+ ndiponso wamkulu wa akuluakulu a boma* oyang’anira amuna onse anzeru a m’Babulo.
9 “‘Iwe Belitesazara mkulu wa ansembe ochita zamatsenga,+ ndikudziwa bwino kuti mzimu wa milungu yoyera uli mwa iwe+ ndipo palibe chinsinsi chimene umavutika nacho.+ Chotero ndiuze zimene ndinaona m’maloto anga ndi kumasulira kwake.+