Danieli 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamene anali kuchita zimenezi, zala za munthu zinaonekera ndipo zinayamba kulemba pafupi ndi choikapo nyale, papulasitala wa pakhoma* la nyumba ya mfumu,+ ndipo mfumuyo inaona dzanja limene linali kulembalo.
5 Pamene anali kuchita zimenezi, zala za munthu zinaonekera ndipo zinayamba kulemba pafupi ndi choikapo nyale, papulasitala wa pakhoma* la nyumba ya mfumu,+ ndipo mfumuyo inaona dzanja limene linali kulembalo.