Miyambo 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mkango, umene ndi wamphamvu kwambiri panyama zonse zakutchire ndiponso umene suopa chilichonse n’kubwerera m’mbuyo,+ Danieli 2:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 inuyo amene Mulungu wakupatsani+ nyama zakutchire ndi mbalame zam’mlengalenga kulikonse kumene kuli anthu, amene Mulungu wakuikani kukhala wolamulira zonsezo, inuyo ndiye mutu wagolide.+ Yoweli 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pali mtundu umene walowa m’dziko langa. Mtunduwo ndi wamphamvu ndipo anthu ake ndi osawerengeka.+ Mano ndiponso nsagwadwa zawo zili ngati za mikango.+
30 Mkango, umene ndi wamphamvu kwambiri panyama zonse zakutchire ndiponso umene suopa chilichonse n’kubwerera m’mbuyo,+
38 inuyo amene Mulungu wakupatsani+ nyama zakutchire ndi mbalame zam’mlengalenga kulikonse kumene kuli anthu, amene Mulungu wakuikani kukhala wolamulira zonsezo, inuyo ndiye mutu wagolide.+
6 Pali mtundu umene walowa m’dziko langa. Mtunduwo ndi wamphamvu ndipo anthu ake ndi osawerengeka.+ Mano ndiponso nsagwadwa zawo zili ngati za mikango.+