Miyambo 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndi bwino kukumana ndi chimbalangondo chimene ana ake asowa,+ kusiyana ndi kukumana ndi chitsiru chochita zopusa.+ Danieli 2:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 “Pambuyo panu padzabwera ufumu wina+ wotsikirapo kwa inu.+ Kenako padzabweranso ufumu wina wachitatu, wamkuwa, umene udzalamulira dziko lonse lapansi.+
12 Ndi bwino kukumana ndi chimbalangondo chimene ana ake asowa,+ kusiyana ndi kukumana ndi chitsiru chochita zopusa.+
39 “Pambuyo panu padzabwera ufumu wina+ wotsikirapo kwa inu.+ Kenako padzabweranso ufumu wina wachitatu, wamkuwa, umene udzalamulira dziko lonse lapansi.+