Danieli 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “PERESI,* ufumu wanu wagawanika ndipo waperekedwa kwa Amedi ndi Aperisiya.”+ Danieli 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Nditakweza maso anga ndinaona nkhosa yamphongo+ itaimirira pafupi ndi mtsinjewo ndipo inali ndi nyanga ziwiri. Nyanga ziwirizi zinali zazitali koma imodzi, imene inamera pomalizira, inali yaitali kuposa inzake.+
3 Nditakweza maso anga ndinaona nkhosa yamphongo+ itaimirira pafupi ndi mtsinjewo ndipo inali ndi nyanga ziwiri. Nyanga ziwirizi zinali zazitali koma imodzi, imene inamera pomalizira, inali yaitali kuposa inzake.+