Genesis 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ufumu wake unayambira ku Babele,+ Ereke,+ Akadi mpaka ku Kaline m’dziko la Sinara.+ Genesis 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamene anthuwo analowera chakum’mawa, anapeza chigwa m’dera la Sinara+ n’kukhazikika kumeneko.