Danieli 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako mmodzi mwa angelowo anafunsa munthu wovala nsalu uja,+ amene anaimirira pamwamba pa madzi a mumtsinjewo, kuti: “Kodi zidzatenga nthawi yaitali bwanji kuti zinthu zodabwitsazi zikwaniritsidwe zonse?”+
6 Kenako mmodzi mwa angelowo anafunsa munthu wovala nsalu uja,+ amene anaimirira pamwamba pa madzi a mumtsinjewo, kuti: “Kodi zidzatenga nthawi yaitali bwanji kuti zinthu zodabwitsazi zikwaniritsidwe zonse?”+