Miyambo 21:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Munthu amene amadzikuza akapsa mtima, amatchedwa wodzikuza, wonyada ndi wodzitama.+ Yesaya 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 chifukwa wolamulira wankhanza adzafika pamapeto pake,+ ndipo wodzitama adzatha.+ Onse okhala tcheru kuti achitire anzawo zoipa+ adzaphedwa,
20 chifukwa wolamulira wankhanza adzafika pamapeto pake,+ ndipo wodzitama adzatha.+ Onse okhala tcheru kuti achitire anzawo zoipa+ adzaphedwa,