Ekisodo 29:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “Zimene uzipereka paguwa lansembelo ndi izi: ana a nkhosa a chaka chimodzi, awiri pa tsiku nthawi zonse.+ Danieli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Kuchokera pa nthawi imene nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse+ zidzachotsedwa,+ ndiponso pamene chinthu chonyansa+ chobweretsa chiwonongeko chidzaikidwa, padzapita masiku 1,290.
38 “Zimene uzipereka paguwa lansembelo ndi izi: ana a nkhosa a chaka chimodzi, awiri pa tsiku nthawi zonse.+
11 “Kuchokera pa nthawi imene nsembe zoyenera kuperekedwa nthawi zonse+ zidzachotsedwa,+ ndiponso pamene chinthu chonyansa+ chobweretsa chiwonongeko chidzaikidwa, padzapita masiku 1,290.