2 Chilombo chimene ndinaonacho chinali ngati nyalugwe,+ koma mapazi ake anali ngati a chimbalangondo,+ ndipo pakamwa pake panali ngati pa mkango.+ Chinjoka+ chija chinapatsa chilombocho mphamvu yake, mpando wake wachifumu, komanso ulamuliro wake waukulu.+