Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pamene ndinali kuyang’anitsitsa nyangazo, ndinaona kuti nyanga ina yaing’ono yamera+ pakati pa nyangazo. Nyanga zitatu pa nyangazi zinazulidwa pamalo amene nyanga yaing’onoyo inamera. Nyangayi inali ndi maso ngati a munthu, ndipo inali ndi pakamwa polankhula mawu odzitukumula.+

  • Chivumbulutso 13:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Chinachitanso zizindikiro zazikulu,+ moti chinapangitsa ngakhale moto kugwera padziko lapansi kuchokera kumwamba, anthu akuona.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena