Danieli 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ponena za nyanga 10 zija, mu ufumuwo mudzatuluka mafumu 10.+ Kenako mudzatulukanso mfumu ina pambuyo pa mafumu amenewa. Mfumuyo idzakhala yosiyana ndi oyambawa+ ndipo idzagonjetsa mafumu atatu.+ Chivumbulutso 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako ndinaona chilombo+ china chikutuluka pansi pa dziko lapansi.+ Chinali ndi nyanga ziwiri ngati mwana wa nkhosa, koma chinayamba kulankhula ngati chinjoka.+
24 Ponena za nyanga 10 zija, mu ufumuwo mudzatuluka mafumu 10.+ Kenako mudzatulukanso mfumu ina pambuyo pa mafumu amenewa. Mfumuyo idzakhala yosiyana ndi oyambawa+ ndipo idzagonjetsa mafumu atatu.+
11 Kenako ndinaona chilombo+ china chikutuluka pansi pa dziko lapansi.+ Chinali ndi nyanga ziwiri ngati mwana wa nkhosa, koma chinayamba kulankhula ngati chinjoka.+