Danieli 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamene ndinali kuyang’anitsitsa nyangazo, ndinaona kuti nyanga ina yaing’ono yamera+ pakati pa nyangazo. Nyanga zitatu pa nyangazi zinazulidwa pamalo amene nyanga yaing’onoyo inamera. Nyangayi inali ndi maso ngati a munthu, ndipo inali ndi pakamwa polankhula mawu odzitukumula.+ Chivumbulutso 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako ndinaona mauthenga atatu onyansa ouziridwa,+ ooneka ngati achule,+ akutuluka m’kamwa mwa chinjoka,+ m’kamwa mwa chilombo,+ ndi m’kamwa mwa mneneri wonyenga.+ Chivumbulutso 20:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ ndi kumumanga zaka 1,000.
8 Pamene ndinali kuyang’anitsitsa nyangazo, ndinaona kuti nyanga ina yaing’ono yamera+ pakati pa nyangazo. Nyanga zitatu pa nyangazi zinazulidwa pamalo amene nyanga yaing’onoyo inamera. Nyangayi inali ndi maso ngati a munthu, ndipo inali ndi pakamwa polankhula mawu odzitukumula.+
13 Kenako ndinaona mauthenga atatu onyansa ouziridwa,+ ooneka ngati achule,+ akutuluka m’kamwa mwa chinjoka,+ m’kamwa mwa chilombo,+ ndi m’kamwa mwa mneneri wonyenga.+
2 Kenako anagwira chinjoka,+ njoka yakale ija,+ amene ndi Mdyerekezi+ ndiponso Satana,+ ndi kumumanga zaka 1,000.