Danieli 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “PERESI,* ufumu wanu wagawanika ndipo waperekedwa kwa Amedi ndi Aperisiya.”+ Danieli 5:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Usiku womwewo, Belisazara mfumu ya Akasidi anaphedwa,+