Danieli 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo Danieli anakalankhula ndi munthu amene anali kuwayang’anira, amene mkulu wa nduna za panyumba ya mfumu+ uja anamuika kuti aziyang’anira Danieli, Hananiya, Misayeli ndi Azariya, ndipo anati:
11 Pamenepo Danieli anakalankhula ndi munthu amene anali kuwayang’anira, amene mkulu wa nduna za panyumba ya mfumu+ uja anamuika kuti aziyang’anira Danieli, Hananiya, Misayeli ndi Azariya, ndipo anati: