Danieli 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno mfumu inauza Asipenazi, mkulu wa nduna za panyumba ya mfumu+ kuti abweretse ena mwa ana a Isiraeli, ana a m’banja lachifumu, ndi ana a anthu olemekezeka,+
3 Ndiyeno mfumu inauza Asipenazi, mkulu wa nduna za panyumba ya mfumu+ kuti abweretse ena mwa ana a Isiraeli, ana a m’banja lachifumu, ndi ana a anthu olemekezeka,+