Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 12:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kenako mmodzi mwa angelowo anafunsa munthu wovala nsalu uja,+ amene anaimirira pamwamba pa madzi a mumtsinjewo, kuti: “Kodi zidzatenga nthawi yaitali bwanji kuti zinthu zodabwitsazi zikwaniritsidwe zonse?”+

  • Chivumbulutso 19:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iye waloledwa kuvala zovala zapamwamba, zonyezimira ndi zoyera bwino, pakuti zovala zapamwambazo zikuimira ntchito zolungama za oyera.”+

  • Chivumbulutso 19:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Komanso magulu ankhondo amene anali kumwamba, anali kumutsatira pamahatchi oyera, atavala zovala zapamwamba, zoyera bwino, za mbee!

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena