Ezekieli 33:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Tsopano madzulo, munthu wopulumuka uja asanafike, dzanja la Yehova linandikhudza.+ Ndipo Mulungu anatsegula pakamwa panga, wopulumuka uja asanafike m’mawa. Pakamwa panga panatseguka ndipo ndinayambanso kulankhula.+
22 Tsopano madzulo, munthu wopulumuka uja asanafike, dzanja la Yehova linandikhudza.+ Ndipo Mulungu anatsegula pakamwa panga, wopulumuka uja asanafike m’mawa. Pakamwa panga panatseguka ndipo ndinayambanso kulankhula.+