Oweruza 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma Yehova anamuuza kuti: “Mtendere ukhale nawe.+ Usachite mantha.+ Suufa.”+ Chivumbulutso 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Nditamuona, ndinagwa pamapazi ake ngati kuti ndafa. Ndipo anandigwira ndi dzanja lake lamanja ndi kundiuza kuti: “Usachite mantha.+ Ine ndine Woyamba+ ndi Wotsiriza,+
17 Nditamuona, ndinagwa pamapazi ake ngati kuti ndafa. Ndipo anandigwira ndi dzanja lake lamanja ndi kundiuza kuti: “Usachite mantha.+ Ine ndine Woyamba+ ndi Wotsiriza,+