-
Danieli 5:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Chifukwa chakuti Mulungu anamupatsa ukulu umenewu, anthu a mitundu yosiyanasiyana, olankhula zinenero zosiyanasiyana anali kunjenjemera ndi kuchita mantha pamaso pake.+ Iye akafuna kupha munthu aliyense anali kumupha, akafuna kuwononga munthu aliyense anali kumuwononga, akafuna kukweza munthu aliyense anali kumukweza ndipo akafuna kutsitsa munthu aliyense anali kumutsitsa.+
-