Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mkwiyo wa mfumu umatanthauza amithenga a imfa,+ koma munthu wanzeru ndi amene amauziziritsa.+

  • Danieli 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mfumu itamva zimenezi inapsa mtima ndipo inakwiya kwambiri,+ moti inanena kuti amuna onse anzeru a m’Babulo ayenera kuphedwa.+

  • Danieli 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Aliyense amene sagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi ndi kulambira fanolo,+ nthawi yomweyo+ aponyedwa m’ng’anjo yoyaka moto.”+

  • Danieli 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsopano ine ndikuika lamulo+ lakuti, anthu onse a mitundu yosiyanasiyana, olankhula zinenero zosiyanasiyana amene anganene chilichonse chotsutsana ndi Mulungu wa Sadirake, Mesake ndi Abedinego ayenera kudulidwa nthulinthuli,+ ndipo nyumba zawo zisandutsidwe zimbudzi za anthu onse,+ pakuti palibe mulungu wina amene amatha kupulumutsa chotere.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena