Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 29:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Anthu onse a ku Yuda amene anatengedwa kupita ku ukapolo ku Babulo, potemberera ena azidzatchula za Zedekiya ndi Ahabu kuti: “Yehova akuchititse kukhala ngati Zedekiya ndi Ahabu+ amene mfumu ya Babulo inawawotcha pamoto!”+

  • Danieli 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Munalamulanso kuti aliyense amene sagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi n’kulambira fanolo aponyedwe m’ng’anjo yoyaka moto.+

  • Danieli 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ngati mungatiponyere m’ng’anjo yoyaka moto, Mulungu wathu amene tikumutumikira akhoza kutipulumutsa. Iye atipulumutsa m’ng’anjo yoyaka moto ndiponso m’manja mwanu mfumu.+

  • Danieli 3:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kenako Nebukadinezara anayandikira khomo la ng’anjo yoyaka motoyo+ ndipo anati: “Sadirake, Mesake ndi Abedinego, inu atumiki a Mulungu Wam’mwambamwamba,+ tulukani ndipo mubwere kuno!” Zitatero, Sadirake, Mesake ndi Abedinego anatuluka pakati pa motopo.

  • Chivumbulutso 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndipo chinaloledwa kupereka mpweya ku chifaniziro cha chilombo chija, kuti chifaniziro cha chilombocho chithe kulankhula, ndi kuchititsa kuti onse amene mwa njira iliyonse salambira chifaniziro+ cha chilombocho, aphedwe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena