Deuteronomo 29:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 munaona zinthu zawo zonyansa ndi mafano awo onyansa,*+ mafano amtengo ndi amwala, asiliva ndi agolide amene anali nawo.) 1 Mafumu 11:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Solomo anayamba kutsatira Asitoreti,+ mulungu wamkazi wa Asidoni, ndi Milikomu,+ chonyansa cha Aamoni. Danieli 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense amene sagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi ndi kulambira fanolo,+ nthawi yomweyo+ aponyedwa m’ng’anjo yoyaka moto.”+ Mateyu 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Choncho, mukadzaona chinthu chonyansa+ chowononga chimene chinanenedwa kudzera mwa mneneri Danieli chitaimirira m’malo oyera,+ (wowerenga adzazindikire,)
17 munaona zinthu zawo zonyansa ndi mafano awo onyansa,*+ mafano amtengo ndi amwala, asiliva ndi agolide amene anali nawo.)
5 Solomo anayamba kutsatira Asitoreti,+ mulungu wamkazi wa Asidoni, ndi Milikomu,+ chonyansa cha Aamoni.
6 Aliyense amene sagwada ndi kuwerama mpaka nkhope yake pansi ndi kulambira fanolo,+ nthawi yomweyo+ aponyedwa m’ng’anjo yoyaka moto.”+
15 “Choncho, mukadzaona chinthu chonyansa+ chowononga chimene chinanenedwa kudzera mwa mneneri Danieli chitaimirira m’malo oyera,+ (wowerenga adzazindikire,)