Danieli 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Itayandikira dzenjelo, inafuulira Danieli ndi mawu achisoni kuti: “Danieli mtumiki wa Mulungu wamoyo, kodi Mulungu wako amene umamutumikira mosalekeza+ wakupulumutsa kwa mikango?”+
20 Itayandikira dzenjelo, inafuulira Danieli ndi mawu achisoni kuti: “Danieli mtumiki wa Mulungu wamoyo, kodi Mulungu wako amene umamutumikira mosalekeza+ wakupulumutsa kwa mikango?”+