Deuteronomo 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Uzikonda Yehova Mulungu wako ndi mtima wako wonse,+ moyo wako wonse,+ ndi mphamvu zako zonse.+ 1 Mbiri 16:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Funafunani Yehova ndiponso mphamvu zake,+Funafunani nkhope yake+ nthawi zonse. Miyambo 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mtima wako usamasirire anthu ochimwa,+ koma iwe uziopa Yehova tsiku lonse.+