Amosi 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yesetsani kuyandikira kwa Yehova, inu a m’nyumba ya Yosefe,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ ndiponso kuti Mulungu asakuyakireni ngati moto.+ Chitani zimenezi kuti motowo usakunyeketseni chifukwa ku Beteli sikungapezeke munthu wouzimitsa.+ Zefaniya 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+
6 Yesetsani kuyandikira kwa Yehova, inu a m’nyumba ya Yosefe,+ kuti mupitirize kukhala ndi moyo+ ndiponso kuti Mulungu asakuyakireni ngati moto.+ Chitani zimenezi kuti motowo usakunyeketseni chifukwa ku Beteli sikungapezeke munthu wouzimitsa.+
3 bwerani kwa Yehova,+ inu nonse ofatsa a padziko lapansi,+ amene mwakhala mukutsatira zigamulo zake. Yesetsani kukhala olungama,+ yesetsani kukhala ofatsa.+ Mwina+ mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+