Salimo 24:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Umenewo ndiwo m’badwo wa amene amafunafuna Mulungu,M’badwo wa anthu ofunafuna nkhope yanu, inu Mulungu wa Yakobo.+ [Seʹlah.] Salimo 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mtima wanga wanena lamulo lanu lakuti: “Ndifunefuneni anthu inu.”+Ndidzakufunafunani, inu Yehova.+ Hoseya 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako ndidzabwerera kumalo anga kufikira iwo atalangidwa chifukwa cha zolakwa zawo+ ndipo adzayamba kufunafuna nkhope yanga.+ Zinthu zikadzawavuta,+ adzandifuna.”+
6 Umenewo ndiwo m’badwo wa amene amafunafuna Mulungu,M’badwo wa anthu ofunafuna nkhope yanu, inu Mulungu wa Yakobo.+ [Seʹlah.]
15 Kenako ndidzabwerera kumalo anga kufikira iwo atalangidwa chifukwa cha zolakwa zawo+ ndipo adzayamba kufunafuna nkhope yanga.+ Zinthu zikadzawavuta,+ adzandifuna.”+