2 Mbiri 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 ndipo anthu anga+ otchedwa ndi dzina langa+ akadzichepetsa+ n’kupemphera,+ n’kufunafuna nkhope yanga,+ n’kusiya njira zawo zoipa,+ ine ndidzamva ndili kumwamba+ n’kuwakhululukira tchimo lawo+ ndipo ndidzachiritsa dziko lawo.+ Yeremiya 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 ‘Mudzaitanira pa ine komanso mudzabwera ndi kupemphera kwa ine ndipo ine ndidzakumvetserani.’+ Hoseya 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo adzayenda motsatira Yehova+ amene adzabangula ngati mkango.+ Inde adzabangula,+ ndipo ana ake adzabwera akunjenjemera kuchokera kumadzulo.+
14 ndipo anthu anga+ otchedwa ndi dzina langa+ akadzichepetsa+ n’kupemphera,+ n’kufunafuna nkhope yanga,+ n’kusiya njira zawo zoipa,+ ine ndidzamva ndili kumwamba+ n’kuwakhululukira tchimo lawo+ ndipo ndidzachiritsa dziko lawo.+
10 Iwo adzayenda motsatira Yehova+ amene adzabangula ngati mkango.+ Inde adzabangula,+ ndipo ana ake adzabwera akunjenjemera kuchokera kumadzulo.+