Levitiko 26:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Zimenezi zinachititsa kuti ine nditsutsane nawo+ ndi kuwatengera kudziko la adani awo.+ “‘Izi zinachitika kuti mwina mitima yawo yosadulidwayo+ ingadzichepetse,+ ndi kulipira chifukwa cha zolakwa zawo. 2 Mbiri 33:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iye atasautsika mumtima mwake chifukwa cha zimenezi,+ anakhazikitsa pansi mtima wa Yehova Mulungu wake+ ndipo anadzichepetsa+ kwambiri pamaso pa Mulungu wa makolo ake. Yakobo 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Dzichepetseni pamaso pa Yehova,+ ndipo iye adzakukwezani.+
41 Zimenezi zinachititsa kuti ine nditsutsane nawo+ ndi kuwatengera kudziko la adani awo.+ “‘Izi zinachitika kuti mwina mitima yawo yosadulidwayo+ ingadzichepetse,+ ndi kulipira chifukwa cha zolakwa zawo.
12 Iye atasautsika mumtima mwake chifukwa cha zimenezi,+ anakhazikitsa pansi mtima wa Yehova Mulungu wake+ ndipo anadzichepetsa+ kwambiri pamaso pa Mulungu wa makolo ake.