Salimo 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mtima wanga wanena lamulo lanu lakuti: “Ndifunefuneni anthu inu.”+Ndidzakufunafunani, inu Yehova.+ Salimo 105:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Funafunani Yehova ndiponso mphamvu zake.+Funafunani nkhope yake nthawi zonse.+