Genesis 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Pa nthawi yoikidwiratu ndidzabweranso kwa iwe chaka chamawa. Ndidzabweranso nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.” Mateyu 19:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Yesu anawayang’anitsitsa n’kunena kuti: “Kwa anthu zimenezi n’zosathekadi, koma zinthu zonse n’zotheka kwa Mulungu.”+ Luka 1:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Izi zachitika chifukwa zimene Mulungu wanena, sizilephereka.”+
14 Kodi pali chosatheka ndi Yehova?+ Pa nthawi yoikidwiratu ndidzabweranso kwa iwe chaka chamawa. Ndidzabweranso nthawi ngati yomwe ino, ndipo Sara adzakhala ndi mwana wamwamuna.”
26 Yesu anawayang’anitsitsa n’kunena kuti: “Kwa anthu zimenezi n’zosathekadi, koma zinthu zonse n’zotheka kwa Mulungu.”+