Ezara 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndaikanso lamulo lakuti aliyense wophwanya+ lamulo limeneli, thabwa+ lidzazulidwa panyumba yake ndipo iye adzapachikidwa+ pathabwalo. Komanso nyumba yake idzasandutsidwa chimbudzi cha aliyense chifukwa cha zimenezi.+
11 Ndaikanso lamulo lakuti aliyense wophwanya+ lamulo limeneli, thabwa+ lidzazulidwa panyumba yake ndipo iye adzapachikidwa+ pathabwalo. Komanso nyumba yake idzasandutsidwa chimbudzi cha aliyense chifukwa cha zimenezi.+