Yesaya 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kubangula kwawo kuli ngati kwa mkango ndipo amabangula ngati mikango yamphamvu.+ Iwo adzabangula n’kugwira nyama. Adzainyamula bwinobwino ndipo sipadzakhala woipulumutsa.+ Amosi 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+
29 Kubangula kwawo kuli ngati kwa mkango ndipo amabangula ngati mikango yamphamvu.+ Iwo adzabangula n’kugwira nyama. Adzainyamula bwinobwino ndipo sipadzakhala woipulumutsa.+
14 Malo othawirapo munthu waliwiro adzawonongeka+ ndipo palibe munthu wamphamvu amene adzalimbe, komanso palibe munthu wamphamvu amene adzapulumutse moyo wake.+