Hoseya 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Gulu la ansembe lakhala gulu la achifwamba.+ Iwo amachita zinthu zofanana ndi za anthu obisalira munthu panjira.+ Amapha anthu m’mphepete mwa njira ku Sekemu+ chifukwa amangokhalira kuchita khalidwe lotayirira.+
9 Gulu la ansembe lakhala gulu la achifwamba.+ Iwo amachita zinthu zofanana ndi za anthu obisalira munthu panjira.+ Amapha anthu m’mphepete mwa njira ku Sekemu+ chifukwa amangokhalira kuchita khalidwe lotayirira.+