-
Deuteronomo 26:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Sindinadyeko zina mwa zimenezi pa nyengo yanga yakulira, kapena kutengapo zina mwa zimenezi ndili wodetsedwa, kapena kupereka gawo lake chifukwa cha munthu wakufa. Ndamvera mawu a Yehova Mulungu wanga. Ndachita mogwirizana ndi zonse zimene munandilamula.
-