Yesaya 57:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Koma anthu inu bwerani pafupi,+ inu ana a mayi wolosera zam’tsogolo,+ mbewu ya munthu wachigololo ndi ya mkazi wochita uhule:+ Yohane 8:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Inu mumachita ntchito za atate wanu.” Iwo anati: “Ife sitinabadwe m’chigololo,* tili ndi Atate mmodzi,+ ndiye Mulungu.”
3 “Koma anthu inu bwerani pafupi,+ inu ana a mayi wolosera zam’tsogolo,+ mbewu ya munthu wachigololo ndi ya mkazi wochita uhule:+
41 Inu mumachita ntchito za atate wanu.” Iwo anati: “Ife sitinabadwe m’chigololo,* tili ndi Atate mmodzi,+ ndiye Mulungu.”