2 Mafumu 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano m’chaka chachinayi cha Mfumu Hezekiya, kutanthauza chaka cha 7 cha Hoshiya+ mwana wa Ela mfumu ya Isiraeli, Salimanesere+ mfumu ya Asuri anabwera ku Samariya n’kuzungulira mzindawo.+ 2 Mafumu 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ili kuti mfumu ya Hamati,+ mfumu ya Aripadi,+ ndi mafumu a mizinda ya Sefaravaimu, Hena, ndi Iva?’”+
9 Tsopano m’chaka chachinayi cha Mfumu Hezekiya, kutanthauza chaka cha 7 cha Hoshiya+ mwana wa Ela mfumu ya Isiraeli, Salimanesere+ mfumu ya Asuri anabwera ku Samariya n’kuzungulira mzindawo.+
13 Ili kuti mfumu ya Hamati,+ mfumu ya Aripadi,+ ndi mafumu a mizinda ya Sefaravaimu, Hena, ndi Iva?’”+