Deuteronomo 32:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kodi sindinasunge zimenezi,Ndi kuziikira chidindo m’nkhokwe yanga?+ Yobu 14:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kulakwa kwanga mwakutsekera m’thumba,+Ndipo mwamata machimo anga ndi zomatira.